By Malawi 24
Bulugama, kaya mandimu oonjeza, mwinanso soda osakaniza ndi khungwa la mtengo wa muwawani ndinso aloe vera ndi zina ndi zina ati muzisiye kaye. Zikukupwetekani izo zija osati kukuthandizani ku nkhondo yolimbana ndi corona. Mkulu amene akutsogolera nkhondo yolimbana ndi kuthana ndi kachilombo ka corona kuno ku Malawi, Dr. Phuka achenjeza a Malawi kuti mchitidwe omwa (…)
The post Chonde, musamwe zitsamba pothana ndi covid – a Dokotala akutelo appeared first on Malawi 24.
Views : 20. Votes : 0. Shares : 0.