By Malawi 24
Mkulu wa chipatala cha Queen Elizabeth mumzinda wa Blantyre walangiza anthu m’dziko muno kuti asakhale ndimantha kupita ku chipatala pomwe akudwala poopa kukawapeza ndi matenda a COVID-19 ndipo ati si aliyense akumamwalira akapita kuchipatala poti ambiri akumachira. Dr Samson Mndolo ati kafukufuku akusonyeza kuti a Malawi ambiri ayamba kuopa kupita kuchipatala pomwe sakumva bwino mthupi (…)
The post Ambiri akumachira akabwera kuchipatala – mkulu wa chipatala cha Queens appeared first on Malawi 2...
Views : 11. Votes : 0. Shares : 0.